Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 15:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Ndiyeno anawauza kuti: “Ngati mudzamveradi mawu a Yehova Mulungu wanu, ndi kuchita zinthu zoyenera pamaso pake ndiponso kumvera malamulo ake ndi kusunga malangizo ake onse,+ sindidzakugwetserani miliri iliyonse imene ndinagwetsera Iguputo,+ chifukwa ine ndine Yehova amene ndikukuchiritsani.”+

  • Levitiko 26:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “‘Mukapitiriza kutsatira malangizo anga ndi kusunga malamulo anga,+

  • Deuteronomo 6:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndipo inu Aisiraeli, muzimvetsera ndi kutsatira mfundo ndi malamulo ake mosamala,+ kuti zinthu zikuyendereni bwino,+ ndi kuti muchuluke kwambiri m’dziko loyenda mkaka ndi uchi, monga mmene Yehova Mulungu wa makolo anu anakulonjezerani.+

  • Yeremiya 11:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Makolo anu ndinawalamula kumvera mawu amenewa pamene ndinali kuwatulutsa m’dziko la Iguputo,+ pamene ndinali kuwatulutsa m’ng’anjo yachitsulo.+ Ndinawalamula kuti, ‘Muzimvera mawu anga, ndipo muzichita zinthu motsatira malamulo onse amene ndakupatsani.+ Mukatero mudzakhaladi anthu anga, ndipo ine ndidzakhala Mulungu wanu,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena