Deuteronomo 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Ndiyeno mukadzamveradi malamulo anga+ amene ndikukupatsani lero, moti n’kukonda Yehova Mulungu wanu ndi kum’tumikira ndi mtima wanu wonse, ndi moyo wanu wonse,+ Mlaliki 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Poti zonse zanenedwa, mfundo yaikulu ndi yakuti: Opa Mulungu woona+ ndi kusunga malamulo ake+ chifukwa zimenezi ndiye zimene munthu ayenera kuchita. Yesaya 48:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Zingakhale bwino kwambiri mutamvera malamulo anga!+ Mukatero mtendere wanu udzakhala ngati mtsinje,+ ndipo chilungamo chanu chidzakhala ngati mafunde a m’nyanja.+
13 “Ndiyeno mukadzamveradi malamulo anga+ amene ndikukupatsani lero, moti n’kukonda Yehova Mulungu wanu ndi kum’tumikira ndi mtima wanu wonse, ndi moyo wanu wonse,+
13 Poti zonse zanenedwa, mfundo yaikulu ndi yakuti: Opa Mulungu woona+ ndi kusunga malamulo ake+ chifukwa zimenezi ndiye zimene munthu ayenera kuchita.
18 Zingakhale bwino kwambiri mutamvera malamulo anga!+ Mukatero mtendere wanu udzakhala ngati mtsinje,+ ndipo chilungamo chanu chidzakhala ngati mafunde a m’nyanja.+