Mlaliki 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ngakhale woipa atachita zoipa+ maulendo 100 n’kukhala ndi moyo wautali akuchitabe zofuna zake, ine ndikudziwa kuti anthu amene amaopa Mulungu woona zidzawayendera bwino,+ chifukwa chakuti anali kumuopa.+ Yesaya 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Amuna inu, nenani kuti anthu olungama zidzawayendera bwino,+ chifukwa adzadya zipatso za zochita zawo.+
12 Ngakhale woipa atachita zoipa+ maulendo 100 n’kukhala ndi moyo wautali akuchitabe zofuna zake, ine ndikudziwa kuti anthu amene amaopa Mulungu woona zidzawayendera bwino,+ chifukwa chakuti anali kumuopa.+
10 Amuna inu, nenani kuti anthu olungama zidzawayendera bwino,+ chifukwa adzadya zipatso za zochita zawo.+