Oweruza 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndichita zimenezi kuti ndiyese+ Isiraeli kudzera mwa mitundu imeneyi, kuti ndione ngati angasunge njira ya Yehova mwa kuyendamo monga mmene makolo awo anachitira, kapena ayi.”
22 Ndichita zimenezi kuti ndiyese+ Isiraeli kudzera mwa mitundu imeneyi, kuti ndione ngati angasunge njira ya Yehova mwa kuyendamo monga mmene makolo awo anachitira, kapena ayi.”