Oweruza 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndichita zimenezi kuti ndiyese Aisiraeli ngati angasunge njira ya Yehova+ poyenda mʼnjirayo ngati mmene makolo awo anachitira.”
22 Ndichita zimenezi kuti ndiyese Aisiraeli ngati angasunge njira ya Yehova+ poyenda mʼnjirayo ngati mmene makolo awo anachitira.”