Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Kodi anthu ena anamvapo mawu a Mulungu akumveka kuchokera pakati pa moto ngati mmene inuyo munawamvera, ndi kukhalabe ndi moyo?+

  • Deuteronomo 5:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ine ndinaima pakati pa Yehova ndi inu pa nthawi imeneyo,+ kuti ndikuuzeni mawu a Yehova, (pakuti munali kuopa moto, ndipo simunakwere m’phirimo).+ Pamenepo iye anati,

  • Salimo 29:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Liwu la Yehova ndi lamphamvu,+

      Liwu la Yehova ndi lokwezeka.+

  • 1 Atesalonika 1:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pakuti iwo amanena mmene ife tinafikira pakati panu koyamba. Amanenanso mmene inu munatembenukira kwa Mulungu, kusiya mafano+ anu kuti mutumikire Mulungu wamoyo+ ndi woona,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena