Deuteronomo 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ine ndinaima pakati pa Yehova ndi inu pa nthawi imeneyo,+ kuti ndikuuzeni mawu a Yehova. Inuyo simunakwere mʼphirimo chifukwa munkaopa moto.+ Ndiyeno Mulungu anati:
5 Ine ndinaima pakati pa Yehova ndi inu pa nthawi imeneyo,+ kuti ndikuuzeni mawu a Yehova. Inuyo simunakwere mʼphirimo chifukwa munkaopa moto.+ Ndiyeno Mulungu anati: