Deuteronomo 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ine ndinaima pakati pa Yehova ndi inu pa nthawi imeneyo,+ kuti ndikuuzeni mawu a Yehova, (pakuti munali kuopa moto, ndipo simunakwere m’phirimo).+ Pamenepo iye anati,
5 Ine ndinaima pakati pa Yehova ndi inu pa nthawi imeneyo,+ kuti ndikuuzeni mawu a Yehova, (pakuti munali kuopa moto, ndipo simunakwere m’phirimo).+ Pamenepo iye anati,