Genesis 47:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yakobo anayankha Farao kuti: “Zaka za moyo wanga monga mlendo m’malo osiyanasiyana zikukwana 130.+ Zaka zimenezi zakhala zowerengeka ndi zosautsa,+ ndipo sizinafike pa zaka za moyo wa makolo anga monga alendo m’malo osiyanasiyana.”+ 1 Mbiri 29:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ifetu ndife alendo pamaso panu, komanso okhala m’dziko la eni+ monga analili makolo athu onse. Masiku athu padziko lapansi ali ngati mthunzi,+ ndipo ndife osakhalitsa. 1 Petulo 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Okondedwa, popeza ndinu alendo ndiponso anthu osakhalitsa m’dzikoli,+ ndikukudandaulirani kuti muzipewa zilakolako za thupi+ zimene zili pa nkhondo yolimbana ndi moyo.+
9 Yakobo anayankha Farao kuti: “Zaka za moyo wanga monga mlendo m’malo osiyanasiyana zikukwana 130.+ Zaka zimenezi zakhala zowerengeka ndi zosautsa,+ ndipo sizinafike pa zaka za moyo wa makolo anga monga alendo m’malo osiyanasiyana.”+
15 Ifetu ndife alendo pamaso panu, komanso okhala m’dziko la eni+ monga analili makolo athu onse. Masiku athu padziko lapansi ali ngati mthunzi,+ ndipo ndife osakhalitsa.
11 Okondedwa, popeza ndinu alendo ndiponso anthu osakhalitsa m’dzikoli,+ ndikukudandaulirani kuti muzipewa zilakolako za thupi+ zimene zili pa nkhondo yolimbana ndi moyo.+