Mateyu 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Odala ndi anthu amene akumva chisoni, chifukwa adzasangalatsidwa.+ Yohane 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndithudi ndikukuuzani, Mudzagwetsa misozi ndi kulira mofuula, koma dzikoli lidzasangalala. Mudzamva chisoni,+ koma chisoni chanu adzachisandutsa chimwemwe.+
20 Ndithudi ndikukuuzani, Mudzagwetsa misozi ndi kulira mofuula, koma dzikoli lidzasangalala. Mudzamva chisoni,+ koma chisoni chanu adzachisandutsa chimwemwe.+