Salimo 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndalefuka chifukwa cha kuusa moyo* kwanga.+Usiku wonse ndimanyowetsa bedi langa.+Ndimakhathamitsa bedi langa ndi misozi.+ Salimo 31:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndikomereni mtima inu Yehova, pakuti ndasautsika kwambiri.+Diso langa lafooka chifukwa cha chisoni,+ chimodzimodzinso moyo wanga ndi m’mimba mwanga.+ Maliro 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndikulirira zinthu zimenezi ngati mkazi.+ Maso anga ine! Maso anga akutuluka misozi.+Pakuti wonditonthoza, munthu woti anditsitsimule, ali kutali ndi ine.Ana anga asiyidwa+ popanda thandizo, pakuti mdani wanga wadzitukumula.+
6 Ndalefuka chifukwa cha kuusa moyo* kwanga.+Usiku wonse ndimanyowetsa bedi langa.+Ndimakhathamitsa bedi langa ndi misozi.+
9 Ndikomereni mtima inu Yehova, pakuti ndasautsika kwambiri.+Diso langa lafooka chifukwa cha chisoni,+ chimodzimodzinso moyo wanga ndi m’mimba mwanga.+
16 Ndikulirira zinthu zimenezi ngati mkazi.+ Maso anga ine! Maso anga akutuluka misozi.+Pakuti wonditonthoza, munthu woti anditsitsimule, ali kutali ndi ine.Ana anga asiyidwa+ popanda thandizo, pakuti mdani wanga wadzitukumula.+