Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 13:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Ndiyeno atangomaliza kulankhula, ana a mfumu aja anafika ndipo anayamba kulira mokweza mawu. Mfumu nayonso pamodzi ndi atumiki ake onse analira kwadzaoneni.

  • Maliro 1:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndikulirira zinthu zimenezi ngati mkazi.+ Maso anga ine! Maso anga akutuluka misozi.+

      Pakuti wonditonthoza, munthu woti anditsitsimule, ali kutali ndi ine.

      Ana anga asiyidwa+ popanda thandizo, pakuti mdani wanga wadzitukumula.+

  • Machitidwe 21:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Koma Paulo anayankha kuti: “N’chifukwa chiyani mukulira+ ndi kunditayitsa mtima?+ Dziwani kuti ine ndine wokonzeka osati kumangidwa kokha, komanso kukafa+ ku Yerusalemu chifukwa cha dzina la Ambuye Yesu.”

  • 2 Akorinto 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Chotero tsopano mukhululukireni ndi mtima wonse+ ndi kumutonthoza, kuopera kuti mwina wotereyu angamezedwe ndi chisoni chake chopitirira malire.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena