2 Akorinto 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kulikonse kumene tikupita, timapirira m’matupi mwathu ndipo timakhala pa ngozi yoti tikhoza kuphedwa, ngati mmene Yesu anachitira,+ kuti moyo wa Yesu uonekerenso m’matupi mwathu.+ 2 Timoteyo 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti ine ndayamba kale kukhuthulidwa ngati nsembe yachakumwa,+ ndipo nthawi yakuti ndimasuke+ yatsala pang’ono kukwana.
10 Kulikonse kumene tikupita, timapirira m’matupi mwathu ndipo timakhala pa ngozi yoti tikhoza kuphedwa, ngati mmene Yesu anachitira,+ kuti moyo wa Yesu uonekerenso m’matupi mwathu.+
6 Pakuti ine ndayamba kale kukhuthulidwa ngati nsembe yachakumwa,+ ndipo nthawi yakuti ndimasuke+ yatsala pang’ono kukwana.