Deuteronomo 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno atsogoleri apitirize kulankhula ndi anthuwo kuti, ‘Kodi pali wamantha ndi wosalimba mtima?+ Achoke ndi kubwerera kunyumba yake, kuti angachititse mantha mitima ya abale ake ngati mmene wachitira mtima wake.’+
8 Ndiyeno atsogoleri apitirize kulankhula ndi anthuwo kuti, ‘Kodi pali wamantha ndi wosalimba mtima?+ Achoke ndi kubwerera kunyumba yake, kuti angachititse mantha mitima ya abale ake ngati mmene wachitira mtima wake.’+