Luka 15:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Chifukwa mwana wanga uyu anali wakufa koma tsopano wakhalanso ndi moyo,+ anatayika koma wapezeka.’ Chotero onse anayamba kukondwerera.
24 Chifukwa mwana wanga uyu anali wakufa koma tsopano wakhalanso ndi moyo,+ anatayika koma wapezeka.’ Chotero onse anayamba kukondwerera.