Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 5:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 “Ndithudi ndikukuuzani, Nthawi idzafika, ndipo ndi inoyi, pamene akufa+ adzamva mawu+ a Mwana wa Mulungu, ndipo olabadirawo adzakhala ndi moyo.+

  • Aroma 6:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndipo musapereke ziwalo zanu ku uchimo+ kuti zikhale zida zochitira zinthu zosalungama,+ koma dziperekeni kwa Mulungu monga anthu amene auka kwa akufa.+ Ziwalo zanunso muzipereke kwa Mulungu monga zida+ zochitira chilungamo.

  • Aefeso 2:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiponso, Mulungu anapangitsa inuyo kukhala amoyo pamene munali akufa chifukwa cha zolakwa zanu ndi machimo anu.+

  • Aefeso 2:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 anatikhalitsa amoyo pamodzi ndi Khristu, ngakhale kuti tinali akufa m’machimo,+ (pakuti inu mwapulumutsidwa chifukwa cha kukoma mtima kwakukulu)+

  • Chivumbulutso 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Kwa mngelo+ wa mpingo wa ku Sade, lemba kuti: Izi ndi zimene akunena iye amene ali ndi mizimu 7+ ya Mulungu, ndi nyenyezi 7.+ ‘Ndikudziwa ntchito zako, kuti uli ndi dzina lakuti uli moyo, pamene ndiwe wakufa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena