Aroma 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndipo musapereke matupi* anu ku uchimo kuti akhale zida zochitira zinthu zosalungama, koma dziperekeni kwa Mulungu ngati anthu amene aukitsidwa. Matupi anunso muwapereke kwa Mulungu ngati zida zochitira chilungamo.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:13 ‘Mulungu Apitirize Kukukondani’, ptsa. 64-65
13 Ndipo musapereke matupi* anu ku uchimo kuti akhale zida zochitira zinthu zosalungama, koma dziperekeni kwa Mulungu ngati anthu amene aukitsidwa. Matupi anunso muwapereke kwa Mulungu ngati zida zochitira chilungamo.+