Maliro 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pa chifukwa chimenechi, mtima wathu wadwala.+ Chifukwa cha zinthu zimenezi, maso athu achita mdima.+
17 Pa chifukwa chimenechi, mtima wathu wadwala.+ Chifukwa cha zinthu zimenezi, maso athu achita mdima.+