Yesaya 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kodi mumenyedwanso pati+ mmene mukupitiriza kupandukamu?+ Mutu wanu uli ndi zilonda zokhazokha, ndipo mtima wanu wafooka.+ Yeremiya 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndagwidwa ndi chisoni chosatha.+ Mtima wanga wadwala. Maliro 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kuipa kwawo konse kuonekere pamaso panu, ndipo muwalange+ koopsa.Muwalange koopsa monga mmene mwandilangira ine chifukwa cha machimo+ anga onse.Pakuti ndikuusa+ moyo kwambiri ndipo mtima wanga ukudwala.+
5 Kodi mumenyedwanso pati+ mmene mukupitiriza kupandukamu?+ Mutu wanu uli ndi zilonda zokhazokha, ndipo mtima wanu wafooka.+
22 Kuipa kwawo konse kuonekere pamaso panu, ndipo muwalange+ koopsa.Muwalange koopsa monga mmene mwandilangira ine chifukwa cha machimo+ anga onse.Pakuti ndikuusa+ moyo kwambiri ndipo mtima wanga ukudwala.+