Maliro 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu ake onse akuusa moyo. Iwo akufunafuna chakudya.+Asinthanitsa zinthu zawo zabwino ndi chakudya kuti adzitsitsimutse.+Inu Yehova ndiyang’aneni. Onani kuti ndakhala ngati mkazi wachabechabe.+
11 Anthu ake onse akuusa moyo. Iwo akufunafuna chakudya.+Asinthanitsa zinthu zawo zabwino ndi chakudya kuti adzitsitsimutse.+Inu Yehova ndiyang’aneni. Onani kuti ndakhala ngati mkazi wachabechabe.+