Salimo 65:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu Wakumva pemphero, anthu a mitundu yonse adzabwera kwa inu.+ Salimo 66:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndithudi, Mulungu wamva,+Wamvetsera mwatcheru mawu a pemphero langa.+