Machitidwe 10:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Mulungu anatumiza mawu kwa Aisiraeli nʼkulengeza kwa iwo uthenga wabwino wa mtendere+ kudzera mwa Yesu Khristu. Ameneyu ndi Ambuye wa onse.+
36 Mulungu anatumiza mawu kwa Aisiraeli nʼkulengeza kwa iwo uthenga wabwino wa mtendere+ kudzera mwa Yesu Khristu. Ameneyu ndi Ambuye wa onse.+