Mateyu 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tsopano Yesu anayandikira nʼkuwauza kuti: “Ulamuliro wonse waperekedwa kwa ine kumwamba ndi padziko lapansi.+ Aroma 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nʼchifukwa chake Khristu anafa nʼkukhalanso ndi moyo, kuti akhale Ambuye wa akufa ndiponso wa amoyo.+ Chivumbulutso 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndinaona kumwamba kutatseguka, kenako ndinaona hatchi yoyera.+ Amene anakwera pahatchiyo dzina lake linali lakuti Wokhulupirika+ ndi Woona.+ Iye amaweruza molungama ndipo akumenya nkhondo mwachilungamo.+ Chivumbulutso 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pamalaya ake akunja komanso pantchafu yake, panalembedwa dzina lakuti, Mfumu ya mafumu ndi Mbuye wa ambuye.+
18 Tsopano Yesu anayandikira nʼkuwauza kuti: “Ulamuliro wonse waperekedwa kwa ine kumwamba ndi padziko lapansi.+
9 Nʼchifukwa chake Khristu anafa nʼkukhalanso ndi moyo, kuti akhale Ambuye wa akufa ndiponso wa amoyo.+
11 Ndinaona kumwamba kutatseguka, kenako ndinaona hatchi yoyera.+ Amene anakwera pahatchiyo dzina lake linali lakuti Wokhulupirika+ ndi Woona.+ Iye amaweruza molungama ndipo akumenya nkhondo mwachilungamo.+
16 Pamalaya ake akunja komanso pantchafu yake, panalembedwa dzina lakuti, Mfumu ya mafumu ndi Mbuye wa ambuye.+