Machitidwe 28:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ena anayamba kukhulupirira+ zimene ananenazo, koma ena sanakhulupirire.+ Aroma 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ngakhale zili choncho, si onse amene analabadira uthenga wabwino.+ Pakuti Yesaya anati: “Yehova, kodi ndani wakhulupirira zimene anamva kwa ife?”+
16 Ngakhale zili choncho, si onse amene analabadira uthenga wabwino.+ Pakuti Yesaya anati: “Yehova, kodi ndani wakhulupirira zimene anamva kwa ife?”+