Yesaya 53:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Kodi ndani wakhulupirira zimene ife tamva?+ Ndipo kodi dzanja la Yehova+ laonetsedwa kwa ndani?+ Yohane 12:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 moti mawu a mneneri Yesaya anakwaniritsidwa. Iye anati: “Yehova,* kodi ndani wakhulupirira zimene ife tamva?+ Ndipo kodi dzanja la Yehova laonetsedwa kwa ndani?”+
38 moti mawu a mneneri Yesaya anakwaniritsidwa. Iye anati: “Yehova,* kodi ndani wakhulupirira zimene ife tamva?+ Ndipo kodi dzanja la Yehova laonetsedwa kwa ndani?”+