Yesaya 53:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Kodi ndani wakhulupirira zimene ife tamva?+ Ndipo kodi dzanja la Yehova+ laonetsedwa kwa ndani?+