Yohane 12:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 moti mawu a mneneri Yesaya anakwaniritsidwa. Iye anati: “Yehova,* kodi ndani wakhulupirira zimene ife tamva?+ Ndipo kodi dzanja la Yehova laonetsedwa kwa ndani?”+ Aroma 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ngakhale zili choncho, si onse amene analabadira uthenga wabwino.+ Pakuti Yesaya anati: “Yehova, kodi ndani wakhulupirira zimene anamva kwa ife?”+
38 moti mawu a mneneri Yesaya anakwaniritsidwa. Iye anati: “Yehova,* kodi ndani wakhulupirira zimene ife tamva?+ Ndipo kodi dzanja la Yehova laonetsedwa kwa ndani?”+
16 Ngakhale zili choncho, si onse amene analabadira uthenga wabwino.+ Pakuti Yesaya anati: “Yehova, kodi ndani wakhulupirira zimene anamva kwa ife?”+