Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 4:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Atatero, anayendayenda+ m’Galileya+ yense kuphunzitsa m’masunagoge+ mwawo, kulalikira uthenga wabwino wa ufumu ndi kuchiritsa anthu matenda amtundu uliwonse+ ndi zofooka zilizonse.

  • Machitidwe 15:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Tsopano atatsutsana kwambiri,+ Petulo anaimirira, ndi kuwauza kuti: “Amuna inu, abale anga, mukudziwa bwino kuti m’masiku oyambirira Mulungu anandisankha ine pakati panu, kuti kudzera pakamwa panga, anthu a mitundu ina amve mawu a uthenga wabwino ndi kukhulupirira.+

  • Akolose 1:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Adzaterodi, malinga ngati mupitirizabe m’chikhulupiriro,+ muli okhazikika pamaziko+ ndiponso olimba, osasunthika+ pa chiyembekezo cha uthenga wabwino umene munamva,+ umenenso unalalikidwa+ m’chilengedwe chonse+ cha pansi pa thambo. Uthenga wabwino umenewu ndi umene ineyo Paulo ndinakhala mtumiki wake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena