Machitidwe 10:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pamenepo Petulo anayamba kulankhula kuti: “Ndazindikira ndithu kuti Mulungu alibe tsankho.+ Machitidwe 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chotero ngati Mulungu anapereka mphatso yaulere imodzimodziyo kwa iwo, monga mmenenso anachitira kwa ife amene tinakhulupirira mwa Ambuye Yesu Khristu,+ ine ndine ndani kuti ndiletse Mulungu?”+
17 Chotero ngati Mulungu anapereka mphatso yaulere imodzimodziyo kwa iwo, monga mmenenso anachitira kwa ife amene tinakhulupirira mwa Ambuye Yesu Khristu,+ ine ndine ndani kuti ndiletse Mulungu?”+