Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 10:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pakuti Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wa milungu+ ndi Mbuye wa ambuye.+ Iye ndi Mulungu wamkulu, wamphamvu ndi woopsa,+ amene sakondera+ munthu aliyense ndipo salandira chiphuphu.+

  • 2 Mbiri 19:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Tsopano mantha+ a Yehova akugwireni.+ Samalani mmene mukuchitira+ chifukwa Yehova Mulungu wathu si wopanda chilungamo+ kapena watsankho,+ ndipo salandira chiphuphu.”+

  • Yobu 34:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Alipo amene sanakonderepo akalonga,

      Ndipo saganizira kwambiri wolemekezeka kuposa wonyozeka,+

      Chifukwa onsewo anapangidwa ndi manja ake.+

  • Aroma 2:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pakuti Mulungu alibe tsankho.+

  • Agalatiya 2:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Tsopano kunena za anthu amene ankaoneka ngati apadera,+ kaya pa chiyambi anali anthu otani, zilibe kanthu kwa ine,+ Mulungu sayang’ana nkhope ya munthu,+ kwa ine, amuna odalirika amenewo sanandiphunzitse kalikonse katsopano.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena