Deuteronomo 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wa milungu+ ndi Mbuye wa ambuye.+ Iye ndi Mulungu wamkulu, wamphamvu ndi woopsa,+ amene sakondera+ munthu aliyense ndipo salandira chiphuphu.+ Machitidwe 10:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pamenepo Petulo anayamba kulankhula kuti: “Ndazindikira ndithu kuti Mulungu alibe tsankho.+ Aroma 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti Mulungu alibe tsankho.+
17 Pakuti Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wa milungu+ ndi Mbuye wa ambuye.+ Iye ndi Mulungu wamkulu, wamphamvu ndi woopsa,+ amene sakondera+ munthu aliyense ndipo salandira chiphuphu.+