Machitidwe 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo Mulungu, amene amadziwa zamumtima,+ anachitira umboni mwa kuwapatsa mzimu woyera,+ monga anachitiranso kwa ife. Agalatiya 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndikufuna mundiuze: Kodi munalandira mzimu+ chifukwa cha ntchito za chilamulo+ kapena chifukwa chokhulupirira zimene munamva?+
8 Ndipo Mulungu, amene amadziwa zamumtima,+ anachitira umboni mwa kuwapatsa mzimu woyera,+ monga anachitiranso kwa ife.
2 Ndikufuna mundiuze: Kodi munalandira mzimu+ chifukwa cha ntchito za chilamulo+ kapena chifukwa chokhulupirira zimene munamva?+