Machitidwe 10:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Pamene Petulo anali kulankhula zinthu izi, mzimu woyera unagwa pa onse amene anali kumvera mawu amenewo.+ Machitidwe 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma nditangoyamba kulankhula, mzimu woyera unawagwera monga mmene unachitiranso pa ife poyamba paja.+
44 Pamene Petulo anali kulankhula zinthu izi, mzimu woyera unagwa pa onse amene anali kumvera mawu amenewo.+
15 Koma nditangoyamba kulankhula, mzimu woyera unawagwera monga mmene unachitiranso pa ife poyamba paja.+