Machitidwe 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo Mulungu, amene amadziwa zamumtima,+ anachitira umboni powapatsa mzimu woyera+ ngati mmene anachitiranso kwa ife.
8 Ndipo Mulungu, amene amadziwa zamumtima,+ anachitira umboni powapatsa mzimu woyera+ ngati mmene anachitiranso kwa ife.