Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 6:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Motero ineyo ndamva kubuula kwa ana a Isiraeli,+ amene Aiguputo akuwagwiritsa ntchito yaukapolo, ndipo ndikukumbukira pangano langa.+

  • Numeri 20:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Potsirizira pake, tinalirira Yehova.+ Iye anamva kulira kwathu, ndipo anatitumizira mngelo+ n’kutitulutsa m’dziko la Iguputo. Tsopano tili kuno ku Kadesi, mzinda umene uli m’malire a dziko lanu.

  • Deuteronomo 26:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Pamenepo tinayamba kufuulira Yehova Mulungu wa makolo athu,+ ndipo Yehova anamva mawu athu+ ndi kuona nsautso yathu, mavuto athu ndi kuponderezedwa kwathu.+

  • Salimo 12:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Tsopano Yehova wanena kuti: “Chifukwa cha kuponderezedwa kwa osautsika, chifukwa cha kuusa moyo kwa anthu osauka,+

      Ndidzanyamuka pa nthawiyo,+

      Ndidzawateteza kwa aliyense wowanyodola.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena