Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 14:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ndiyeno mngelo+ wa Mulungu woona amene anali kuyenda patsogolo pa Aisiraeli anachoka n’kupita kumbuyo kwawo. Motero, mtambo woima njo ngati chipilala uja unachoka kutsogolo n’kukaima kumbuyo kwawo.+

  • Ekisodo 23:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “Tsopano ndikukutumizira mngelo+ wokutsogolera kuti akuteteze m’njira ndi kukakulowetsa m’dziko limene ndakukonzera.+

  • Ekisodo 33:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndipo ndidzatumiza mngelo patsogolo panu+ kuti akathamangitse Akanani, Aamori, Ahiti, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi.+

  • Machitidwe 7:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Mose ameneyo, amene iwo anamukana ndi kunena kuti, ‘Iweyo anakuika ndani kuti ukhale wolamulira ndi woweruza wathu?’+ munthu ameneyo ndi amene Mulungu anamutumiza+ monga wolamulira ndi mpulumutsi kudzera mwa mngelo amene anaonekera kwa iye pachitsamba chaminga chija.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena