Ekisodo 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Poyankha iye anati: “Anakuika iwe ndani kukhala kalonga ndi woweruza wathu?+ Kodi ukufuna kundipha mmene unaphera Mwiguputo uja?”+ Pamenepo Mose anachita mantha ndipo anati mumtima mwake: “Haa! Nkhani ija yadziwika.”+ Machitidwe 7:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma amene anali kuzunza mnzakeyo anamukankha ndi kunena kuti, ‘Iweyo anakuika ndani kuti ukhale wolamulira ndi woweruza wathu?+
14 Poyankha iye anati: “Anakuika iwe ndani kukhala kalonga ndi woweruza wathu?+ Kodi ukufuna kundipha mmene unaphera Mwiguputo uja?”+ Pamenepo Mose anachita mantha ndipo anati mumtima mwake: “Haa! Nkhani ija yadziwika.”+
27 Koma amene anali kuzunza mnzakeyo anamukankha ndi kunena kuti, ‘Iweyo anakuika ndani kuti ukhale wolamulira ndi woweruza wathu?+