Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 48:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Mngelo amene wakhala akundiwombola ku masoka anga onse,+ adalitse anyamatawa.+

      Dzina langa ndi mayina a makolo anga, Abulahamu ndi Isaki, apitirize kutchulidwa kudzela mwa anawa,+

      Komanso, anawa adzachulukane, adzakhale khamu la anthu padziko lapansi.”+

  • Ekisodo 32:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Tsopano atsogolere anthuwa kumalo amene ndakuuza. Taona! Mngelo wanga akhala patsogolo panu,+ ndipo pa tsiku langa lopereka chilango, ndidzawalangadi chifukwa cha tchimo lawo.”+

  • Numeri 20:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Potsirizira pake, tinalirira Yehova.+ Iye anamva kulira kwathu, ndipo anatitumizira mngelo+ n’kutitulutsa m’dziko la Iguputo. Tsopano tili kuno ku Kadesi, mzinda umene uli m’malire a dziko lanu.

  • Yuda 9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma pamene Mikayeli+ mkulu wa angelo+ anasemphana maganizo+ ndi Mdyerekezi ndipo anakangana naye za mtembo wa Mose,+ sanayese n’komwe kumuweruza ndi mawu onyoza,+ m’malomwake anati: “Yehova akudzudzule.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena