Ekisodo 23:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Tsopano ndikukutumizira mngelo+ wokutsogolera kuti akuteteze m’njira ndi kukakulowetsa m’dziko limene ndakukonzera.+ Ekisodo 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo ndidzatumiza mngelo patsogolo panu+ kuti akathamangitse Akanani, Aamori, Ahiti, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi.+
20 “Tsopano ndikukutumizira mngelo+ wokutsogolera kuti akuteteze m’njira ndi kukakulowetsa m’dziko limene ndakukonzera.+
2 Ndipo ndidzatumiza mngelo patsogolo panu+ kuti akathamangitse Akanani, Aamori, Ahiti, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi.+