Amosi 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ‘Pa tsiku limene ndidzalanga Isiraeli+ chifukwa cha kupanduka kwake, ndidzaperekanso chiweruzo pamaguwa ansembe a ku Beteli+ ndipo nyanga za guwa lansembe zidzazulidwa ndi kugwa pansi.+ Aroma 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma chifukwa chakuti ndiwe wosafuna kusintha khalidwe+ ndiponso wa mtima wosalapa,+ ukudzisungira mkwiyo wa Mulungu.+ Mulungu adzasonyeza mkwiyo+ umenewu pa tsiku loulula+ chiweruzo chake cholungama.+
14 ‘Pa tsiku limene ndidzalanga Isiraeli+ chifukwa cha kupanduka kwake, ndidzaperekanso chiweruzo pamaguwa ansembe a ku Beteli+ ndipo nyanga za guwa lansembe zidzazulidwa ndi kugwa pansi.+
5 Koma chifukwa chakuti ndiwe wosafuna kusintha khalidwe+ ndiponso wa mtima wosalapa,+ ukudzisungira mkwiyo wa Mulungu.+ Mulungu adzasonyeza mkwiyo+ umenewu pa tsiku loulula+ chiweruzo chake cholungama.+