Ekisodo 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova anali kuyenda patsogolo pawo mumtambo woima njo ngati chipilala powatsogolera usana,+ ndipo usiku anali kuwatsogolera m’moto woima njo ngati chipilala kuti uziwaunikira, kuti apitirizebe ulendo usana ndi usiku.+ Salimo 34:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mngelo wa Yehova amamanga msasa mozungulira onse oopa Mulungu,+Ndipo amawapulumutsa.+ Yesaya 52:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu inu simudzatuluka mwachipwirikiti, komanso simudzachoka chothawa.+ Pakuti Yehova azidzayenda patsogolo panu,+ ndipo Mulungu wa Isiraeli azidzalondera kumbuyo kwanu.+
21 Yehova anali kuyenda patsogolo pawo mumtambo woima njo ngati chipilala powatsogolera usana,+ ndipo usiku anali kuwatsogolera m’moto woima njo ngati chipilala kuti uziwaunikira, kuti apitirizebe ulendo usana ndi usiku.+
12 Anthu inu simudzatuluka mwachipwirikiti, komanso simudzachoka chothawa.+ Pakuti Yehova azidzayenda patsogolo panu,+ ndipo Mulungu wa Isiraeli azidzalondera kumbuyo kwanu.+