Ekisodo 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova anali kuyenda patsogolo pawo mumtambo woima njo ngati chipilala powatsogolera usana,+ ndipo usiku anali kuwatsogolera m’moto woima njo ngati chipilala kuti uziwaunikira, kuti apitirizebe ulendo usana ndi usiku.+ Deuteronomo 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 chifukwa Yehova Mulungu wanu akuyenda limodzi nanu kuti akumenyereni nkhondo ndi kukupulumutsani kwa adani anu.’+ 1 Mbiri 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno ukakamva phokoso la kuguba pamwamba pa zitsamba za baka,+ ukatuluke n’kumenyana nawo+ chifukwa Mulungu woona adzakhala atatsogola+ kukapha gulu lankhondo la Afilisiti.”
21 Yehova anali kuyenda patsogolo pawo mumtambo woima njo ngati chipilala powatsogolera usana,+ ndipo usiku anali kuwatsogolera m’moto woima njo ngati chipilala kuti uziwaunikira, kuti apitirizebe ulendo usana ndi usiku.+
4 chifukwa Yehova Mulungu wanu akuyenda limodzi nanu kuti akumenyereni nkhondo ndi kukupulumutsani kwa adani anu.’+
15 Ndiyeno ukakamva phokoso la kuguba pamwamba pa zitsamba za baka,+ ukatuluke n’kumenyana nawo+ chifukwa Mulungu woona adzakhala atatsogola+ kukapha gulu lankhondo la Afilisiti.”