Oweruza 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamenepo mkwiyo wa Yehova unayakira Isiraeli,+ moti anawapereka m’manja mwa ofunkha, ndipo anayamba kufunkha zinthu zawo.+ Iye anawagulitsa kwa adani awo owazungulira+ moti sanathe kuima pamaso pa adani awo.+ Oweruza 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mulungu anapitirizabe kugwiritsa ntchito mitunduyo poyesa+ Aisiraeli, kuti aone ngati Aisiraeliwo adzamvera malamulo a Yehova amene anaperekedwa kwa makolo awo kudzera mwa Mose.+ Salimo 89:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Palibe mdani amene adzamupondereza,+Ndipo palibe mwana aliyense wa anthu oipa amene adzamusautsa.+
14 Pamenepo mkwiyo wa Yehova unayakira Isiraeli,+ moti anawapereka m’manja mwa ofunkha, ndipo anayamba kufunkha zinthu zawo.+ Iye anawagulitsa kwa adani awo owazungulira+ moti sanathe kuima pamaso pa adani awo.+
4 Mulungu anapitirizabe kugwiritsa ntchito mitunduyo poyesa+ Aisiraeli, kuti aone ngati Aisiraeliwo adzamvera malamulo a Yehova amene anaperekedwa kwa makolo awo kudzera mwa Mose.+
22 Palibe mdani amene adzamupondereza,+Ndipo palibe mwana aliyense wa anthu oipa amene adzamusautsa.+