2 Samueli 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye ndi amene adzamangira dzina langa nyumba,+ ndipo ndidzakhazikitsa mpando wake wachifumu mpaka kalekale.+ 1 Mbiri 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo anthu anga Aisiraeli ndidzawasankhira malo ndi kuwakhazika pamalowo.+ Iwo adzakhaladi kumeneko ndipo sadzasokonezedwanso. Anthu osalungama+ sadzawavutitsanso ngati mmene anachitira poyamba,+ Mateyu 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo Mdyerekezi uja anamusiya,+ ndipo kunabwera angelo ndi kuyamba kum’tumikira.+
13 Iye ndi amene adzamangira dzina langa nyumba,+ ndipo ndidzakhazikitsa mpando wake wachifumu mpaka kalekale.+
9 Ndipo anthu anga Aisiraeli ndidzawasankhira malo ndi kuwakhazika pamalowo.+ Iwo adzakhaladi kumeneko ndipo sadzasokonezedwanso. Anthu osalungama+ sadzawavutitsanso ngati mmene anachitira poyamba,+