Deuteronomo 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Nthawi zonse uzikonda Yehova Mulungu wako+ ndi kuchita zofuna zake, kutsatira mfundo zake, zigamulo zake+ ndi malamulo ake. Deuteronomo 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Awa ndi malangizo+ ndi zigamulo+ zimene muyenera kuzitsatira mosamala,+ masiku onse amene mudzakhala m’dziko limene Yehova Mulungu wa makolo anu adzakulolani kuti mulitenge kukhala lanu.+
11 “Nthawi zonse uzikonda Yehova Mulungu wako+ ndi kuchita zofuna zake, kutsatira mfundo zake, zigamulo zake+ ndi malamulo ake.
12 “Awa ndi malangizo+ ndi zigamulo+ zimene muyenera kuzitsatira mosamala,+ masiku onse amene mudzakhala m’dziko limene Yehova Mulungu wa makolo anu adzakulolani kuti mulitenge kukhala lanu.+