Levitiko 19:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Muzisunga malangizo anga onse ndi zigamulo zanga zonse, ndipo muzizitsatira.+ Ine ndine Yehova.’” Levitiko 25:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Muzisunga malangizo anga ndi zigamulo zanga. Mukatero mudzakhala otetezeka m’dzikolo.+