1 Mbiri 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo anthu anga Aisiraeli ndidzawasankhira malo ndi kuwakhazika pamalowo.+ Iwo adzakhaladi kumeneko ndipo sadzasokonezedwanso. Anthu osalungama+ sadzawavutitsanso ngati mmene anachitira poyamba,+
9 Ndipo anthu anga Aisiraeli ndidzawasankhira malo ndi kuwakhazika pamalowo.+ Iwo adzakhaladi kumeneko ndipo sadzasokonezedwanso. Anthu osalungama+ sadzawavutitsanso ngati mmene anachitira poyamba,+