8 Chotero ngati dzanja lako kapena phazi lako limakupunthwitsa, ulidule ndi kulitaya kutali.+ Ndi bwino kuti ukapeze moyo ulibe chiwalo chimodzi kapena uli wolumala kusiyana ndi kuti ukaponyedwe m’moto wosatha uli ndi manja onse awiri kapena mapazi onse awiri.+