Ezekieli 24:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “‘Unachita zonyansa chifukwa cha khalidwe lako lotayirira.+ Ine ndinayesetsa kukuyeretsa, koma zonyansa zako sizinachoke.+ Sudzayeranso kufikira nditathetsera mkwiyo wanga pa iwe.+ Hoseya 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kunyada kwa Isiraeli kwakhala umboni womutsutsa,+ koma iwo sanabwerere kwa Yehova Mulungu wawo.+ Sanamufunefune ngakhale kuti achita zinthu zonsezi.+
13 “‘Unachita zonyansa chifukwa cha khalidwe lako lotayirira.+ Ine ndinayesetsa kukuyeretsa, koma zonyansa zako sizinachoke.+ Sudzayeranso kufikira nditathetsera mkwiyo wanga pa iwe.+
10 Kunyada kwa Isiraeli kwakhala umboni womutsutsa,+ koma iwo sanabwerere kwa Yehova Mulungu wawo.+ Sanamufunefune ngakhale kuti achita zinthu zonsezi.+