Yeremiya 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho mvula yamvumbi yasiya kugwa,+ ndipo mvula yomalizira siinagwe.+ Ukuchita zinthu mopanda manyazi ngati mkazi amene akuchita uhule.* Palibe chimene chikukuchititsa manyazi.+ Hoseya 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kunyada kwa Isiraeli kwakhala umboni womutsutsa,+ ndipo Isiraeli ndi Efuraimu apunthwa ndi zochita zawo.+ Nayenso Yuda wapunthwa pamodzi nawo.+
3 Choncho mvula yamvumbi yasiya kugwa,+ ndipo mvula yomalizira siinagwe.+ Ukuchita zinthu mopanda manyazi ngati mkazi amene akuchita uhule.* Palibe chimene chikukuchititsa manyazi.+
5 Kunyada kwa Isiraeli kwakhala umboni womutsutsa,+ ndipo Isiraeli ndi Efuraimu apunthwa ndi zochita zawo.+ Nayenso Yuda wapunthwa pamodzi nawo.+